Acts 25:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Omneneza aja ataimirira, sadamneneze choipa nchimodzi chomwe pa zimene ndinkaganiza ine.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene anaimirira omneneza, sanamtchulira konse chifukwa cha zoipa zonga ndinazilingirira ine;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Omuyimba mlandu aja atayimirira kuti ayankhule, iwo sananene cholakwa chilichonse chimene ndimayembekezera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene anaimirira omneneza, sanamchulira konse cifukwa ca zoipa zonga ndinazilingirira ine;