Acts 25:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Paulo adapempha kuti abasungidwa m'ndende mpaka Mfumu ya ku Roma itatsimikiza za mlandu wake. Pamenepo ndidalamula kuti amsunge m'ndende kufikira nditamtumiza kwa Mfumuyo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma pakunena Paulo ndi kuti, asungidwe, akatulukire kwa Augusto, ndinaweruza asungidwe iye kufikira ndikamtumiza kwa Kaisara.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Paulo anapempha kuti akaonekere pamaso pa mfumu ya Chiroma, ndipo ndinalamula kuti asungidwe mpaka pamene ndidzamutumize kwa Kaisara.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma pakunena Paulo ndi kuti, asungidwe, akaturukire kwa Augusto, ndinaweruza asungidwe iye kufikira ndikamtumiza kwa Kaisara.