Acts 25:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuti aŵakomere mtima pakumtumiza Paulo ku Yerusalemu. Adaatero chifukwa anali atapangana zomulalira Paulo kuti amuphe pa njira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nampempha kuti mlandu wake wa Paulo uipe, kuti amuitane iye adze ku Yerusalemu; iwo amchitira chifwamba kuti amuphe panjira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anamupempha Festo kuti awakomere mtima potumiza Paulo ku Yerusalemu, pakuti anali atakonzekera chiwembu kuti amuphe Pauloyo pa njira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nampempha kuti mlandu wace wa Paulo uipe, kuti amuitane iye adze ku Yerusalemu; iwo amcitira cifwamba kuti amuphe panjira.