Acts 25:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paulo poyankha zomnenezazo adati, “Ine sindidalakwirepo Malamulo a Ayuda, kapena Nyumba ya Mulungu, kapenanso Mfumu ya ku Roma.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma Paulo podzikanira ananena, Sindinachimwa kanthu kapena pachilamulo cha Chiyuda, kapena pa Kachisi, kapena pa Kaisara.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Paulo ananena mawu ake odziteteza kuti, “Ine sindinalakwirepo lamulo la Ayuda, kapena Nyumba ya Mulungu kapenanso Kaisara.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma Paulo podzikanira ananena, Sindinacimwa kanthu kapena pacilamulo, kapena paKacisi, kapena pa Kaisara.