Acts 26:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa cha zimenezi Ayuda adandigwira m'Nyumba ya Mulungu nafuna kundipha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa cha izi Ayuda anandigwira m'Kachisi, nayesa kundipha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ichi nʼchifukwa chake Ayuda anandigwira mʼbwalo la Nyumba ya Mulungu nafuna kundipha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa ca izi Ayuda anandigwira m'Kacisi, nayesa kundipha.