Acts 26:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Paulo ankadziteteza ku zomnenezazo, Fesito adanena mokweza mau kuti, “Misalatu imeneyi, iwe Paulo! Kuphunziritsa kwako kukukupengetsa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma pakudzikanira momwemo, Fesito anati ndi mau akulu, Uli wamisala Paulo; kuwerengetsa kwako kwakuchititsa misala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Paulo akudziteteza, Festo anakweza mawu nati, “Wazungulira mutu Paulo! Kuphunzira kwako kwakuchititsa misala.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma pakudzikanira momwemo, Festo anati ndi mau akuru, Uli wamisala Paulo; kuwerengetsa kwako kwakucititsa misala.