Acts 26:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mfumu Agripa, kodi mumakhulupirira mau a aneneri? Ndikudziŵa kuti mumaŵakhulupirira.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mfumu Agripa, mukhulupirira aneneri kodi? Ndidziwa kuti muwakhulupirira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu Agripa, kodi mumakhulupirira mawu a aneneri? Ine ndikudziwa kuti mumakhulupirira.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mfumu Agripa, mukhulupirira aneneri kodi? ndidziwa kuti muwakhulupirira.