Acts 26:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Agripa adauza Paulo kuti, “Uganiza kuti nkundisandutsa mkhristu pa kanthaŵi kochepa, komweka?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Agripa anati kwa Paulo, Ndi kundikopa pang'ono ufuna kundiyesera mkhristu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Agripa anati kwa Paulo, “Kodi ukuganiza kuti mʼkanthawi kochepa kotere ungandikope kuti ndikhale Mkhristu?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Agripa anati kwa Paulo, Ndi kundikopa pang'ono ufuna kundiyesera Mkristu.