Acts 26:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo mfumu Agripa, bwanamkubwa, Berenise, ndi onse amene anali nawo adaimirira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ananyamuka mfumu, ndi kazembe, ndi Berenise, ndi iwo akukhala nao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu inayimirira pamodzi ndi bwanamkubwa ndi Bernisi ndiponso anthu onse amene anakhala nawo pamodzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ananyamuka mfumu, ndi kazembe, ndi Bemike, ndi iwo akukhala nao;