Acts 26:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Bwanji ena mwa inu Ayuda mumayesa kuti nkosatheka kukhulupirira kuti Mulungu nkuukitsa anthu kwa akufa?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muchiyesa chinthu chosakhulupirika, chakuti Mulungu aukitsa akufa?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chiyani ena a inu mukuganiza kuti nʼkosatheka kuti Mulungu aukitse akufa?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muciyesa cinthu cosakhulupirika, cakuti Mulungu aukitsa akufa?