Acts 27:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Abale, ine ndikuwona kuti pa ulendowu zinthu zambiri zidzawonongeka ndi kutayika, osati katundu yekha ndi chombo ai, komanso moyo wathu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nanena nao, Amuna inu, ndiona ine kuti ulendo udzatitengera kuonongeka ndi kutayika kwambiri, si kwa akatundu okha kapena ngalawa yokha, komatunso kwa moyo wathu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Anthu inu, ine ndikuona kuti ulendo wathuwu ukhala woopsa ndipo katundu ndi sitima ziwonongeka, ngakhalenso miyoyo yathu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nanena nao, Amuna inu, ndiona ine kuti ulendo udzatitengera kuonongeka ndi kutayika kwambiri, si kwa akatundu okha kapena ngalawa yokha, komatunso kwa moyo wathu.