Acts 27:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tidafika pafupi ndi kachilumba kotchedwa Kauda, ku mbali yosawombapo mphepo. Kumeneko movutikira tidatha kuwongolera kabwato kokokedwa ndi chombo chija.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo popita kuseri kwa chisumbu chaching'ono dzina lake Kauda, tinakhoza kumangitsa bwato koma movutika;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tikudutsa mʼmbali mwa kachilumba kakangʼono kotchedwa Kawuda, tinavutika kuti tisunge bwato lopulumukiramo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo popita kutseri kwa cisumbu cacing'ono dzina lace Kauda, tinakhoza kumangitsa bwato koma mobvutika;