Acts 27:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Popeza kuti tinkavutika naye kwambiri namondweyo, m'maŵa mwake adayamba kutaya katundu m'madzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo povutika kwakukulu ndi namondweyo, m'mawa mwake anayamba kutaya akatundu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ife tinavutika kwambiri ndi namondwe kotero kuti mmawa mwake tinayamba kuponya katundu mʼmadzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pobvutika kwakukuru ndi namondweyo, m'mawa mwace anayamba kutaya akatundu;