Acts 27:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono atayesa kuzama kwa nyanja, adapeza mamita 37. Atayenda pang'ono, adayesanso napeza mamita 27.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo anayesa madzi, napeza mikwamba makumi awiri; ndipo katapita kanthawi, anayesanso, napeza mikwamba khumi ndi isanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anatenga choyezera kuzama kwa nyanja ndi kupeza kuti kuzama kwake kunali mamita 36. Atayendanso pangʼono anatenganso choyezera chija napeza kuti kuzama kwake kunali 27.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo anayesa madzi, napeza mikwamba makumi awiri; ndipo katapita kanthawi, anayesanso, napeza mikwamba khumi ndi isanu.