Acts 27:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Paulo adauza mtsogoleri wa asilikali uja, pamodzi ndi asilikali ake omwe kuti, “Ngati anthu aŵa sakhala m'chombo muno, ndithu inu simutha kupulumuka ai.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Paulo anati kwa kenturiyo ndi kwa asilikali, Ngati awa sakhala m'ngalawa inu simukhoza kupulumuka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo Paulo anawuza wolamulira asilikali uja ndi asilikaliwo kuti, “Ngati anthu awa sakhala mʼsitima muno, inu simungapulumuke.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Paulo anati kwa kenturiyo ndi kwa asilikari, Ngati awa sakhala m'ngalawa inu simukhoza kupulumuka.