Acts 27:38 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Onse aja atadya nkukhuta, adapeputsa chombo pakutaya tirigu m'nyanja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo m'mene anakhuta, anapepuza ngalawa, nataya tirigu m'nyanja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Onse atadya, nakhuta anapeputsa sitimayo potaya tirigu mʼnyanja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo m'mene anakhuta, anapepuza ngalawa, nataya tirigu m'nyarija.