Acts 27:42 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Asilikali aja adaganiza zakupha akaidi, kuwopa kuti ena mwa iwo angasambire kukafika ku mtunda nkuthaŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo uphungu wa asilikali udati awaphe andende, angasambire, ndi kuthawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Asilikali anaganiza za kupha amʼndende onse, kuti angasambire kupita pa mtunda ndi kuthawa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo uphungu wa asilikari udati awapheandende, angasambire, ndi kuthawa.