Acts 27:44 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Otsalawo adaŵalamula kuti agwire matabwa kapena zina za chombo choswekacho. Motero onse adapulumuka nakafika kumtunda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo otsalawo, ena pamatabwa, ndi ena pa zina za m'ngalawa. Ndipo kudatero kuti onse adapulumukira pamtunda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Otsalawo anayenera kugwira matabwa kapena tizidutswa ta sitimayo. Motero onse anapulumuka nakafika pa mtunda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo otsalawo, ena pamatabwa, ndi ena pa zina za m'ngalawa. Ndipo kudatero kuti lonse adapulumukira pamtunda.