Acts 27:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tidawoloka nyanja mbali ya ku Silisiya ndi Pamfiliya nkumafika ku Mira, mzinda wa ku Likiya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene tidapyola nyanja ya kunsi kwake kwa Silisiya ndi Pamfiliya, tinafika ku Mira wa Likiya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Titawoloka nyanja mbali ya gombe la Kilikiya ndi Pamfiliya, tinakafika ku Mura, mzinda wa ku Lukia.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene tidapyola nyanja ya kunsi kwace kwa Kilikiya ndi Pamfiliya, tinafika ku Mura wa Lukiya.