Acts 27:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tidayenda movutikira m'mbali mwa chilumbacho, nkukafika ku malo ena otchedwa Madooko Okoma, pafupi ndi mzinda wa Lasea.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo popazapazapo movutika, tinafika kumalo ena dzina lake Pokocheza Pokoma; pafupi pamenepo panali mudzi wa Lasea.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Timayenda movutikira mʼmbali mwa chilumbacho ndipo tinafika pa malo wotchedwa Madooko Okoma, pafupi ndi mzinda wa Laseya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo popaza-pazapo mobvutika, tinafika ku malo ena dzina lace Pokoceza Pokoma; pafupi pamenepo panali mudzi wa Laseya.