Acts 28:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu aja adatipatsa mphatso zambiri, ndipo pamene tidanyamukanso ulendo wathu wapachombo, adatipatsa zonse zosoŵeka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
amenenso anatichitira ulemu wambiri; ndipo pochoka ife anatiikira zotisowa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthuwo anatilemekeza ife mʼnjira zambiri ndipo pamene tinakonzeka kuti tiyambe ulendo, anatipatsa zonse zomwe tinazisowa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
amenenso anaticitira ulemu wambiri; ndipo pocoka ife anatiikira zotisowa.