Acts 28:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo atandifunsa, adaafuna kundimasula, chifukwa sadapeze mlandu woyenera kundiphera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndiwo, atandifunsafunsa ine anafuna kundimasula, popeza panalibe chifukwa cha kundiphera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anandifufuza ndipo anafuna kundimasula chifukwa sanandipeze wopalamula mlandu woyenera kuphedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndiwo, atandifunsafunsa ine anafuna kundimasula, popeza panalibe cifukwa ca kundiphera.