Acts 28:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma makamaka nkwabwino kuti mutiwuze maganizo anu, pakuti za gulu lanu lopatulikali tikudziŵa kuti ponseponse anthu akutsutsana nalo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma tifuna kumva mutiuze muganiza chiyani; pakuti za mpatuko uwu, tidziwa kuti aunenera ponseponse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ife tikufuna kumva maganizo ako ndi otani, pakuti tikudziwa kuti ponseponse anthu akuyankhula zotsutsana ndi mpatuko umenewu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma tifuna kumva mutiuze muganiza ciani; pakuti za mpatuko uwu, tidziwa kuti aunenera ponse ponse.