Acts 28:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“ ‘Pita kwa anthu a mtundu uwu ndi kuŵauza kuti: Kumva mudzamva, koma osamvetsa, kupenya mudzapenya, koma osazindikira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kuti, Pita kwa anthu awa, nuti, Ndi kumva mudzamva, ndipo simudzazindikira konse; ndipo pakupenya mudzapenya, koma osaona konse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Pita kwa anthu awa ndi kuwawuza kuti, ‘Kumva mudzamva, koma osamvetsetsa; kupenya mudzapenya, koma osaona kanthu.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kuti, Pita kwa anthu awa, nuti, Ndi kumva mudzamva, ndipo simudzazindikira konse; Ndipo pakupenya mudzapenya, koma osaona konse;