Acts 28:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paulo adakatola nkhuni nabwerako ndi mtolo, ndipo pamene ankaziika pa moto, mumtolomo mudatuluka mphiri chifukwa cha kutenthako. Idamluma nkukanirira ku dzanja lakelo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma pamene Paulo adaola chisakata cha nkhuni, nachiika pamoto, inatulukamo njoka, chifukwa cha kutenthaku, niluma dzanja lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Paulo anatola mtolo wankhuni, pamene amayika pa moto, munatulukamo njoka chifukwa cha kutentha, ndipo inamuluma pa dzanja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma pamene Paulo adaola cisakata ca nkhuni, naciika pamoto, inaturukamo njoka, cifukwa ca kutenthaku, nilumadzanja lace.