Acts 28:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Paulo adakhala kumeneko zaka ziŵiri zathunthu m'nyumba yake yobwereka, ndipo ankaŵalandira bwino lomwe onse obwera kudzamuwona.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anakhala zaka ziwiri zamphumphu m'nyumba yake yobwereka, nalandira onse akufika kwa iye,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Paulo anakhala kumeneko zaka ziwiri zathunthu mʼnyumba yobwereka yomwe amalipira ndipo ankalandira aliyense amene amabwera kudzamuona.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anakhala zaka ziwiri zamphumphu m'nyumba yace yobwereka, nalandira onse akufika kwa iye,