Acts 28:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pafupi ndi malowo panali minda ya Publio, mkulu wa pachilumbapo. Iye adatilandira natisamala bwino masiku atatu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma pafupi pamenepo panali minda, mwini wake ndiye mkulu chisumbucho, dzina lake Publio; amene anatilandira ife, natichereza okoma masiku atatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pafupi ndi malowa panali munda wa Popliyo, mkulu wa boma la pa chilumbacho. Iye anatilandira natisamala bwino masiku atatu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma pafupt pamenepo panali minda, mwini wace ndiye mkulu cisumbuco, dzina lace Popliyo; amene anatilandira ife, naticereza okoma masiku atatu.