Acts 4:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono poonanso munthu wochiritsidwa uja ataimirira pafupi ndi Petro ndi Yohane, adasoŵa poŵatsutsira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipotu pakuona munthu wochiritsidwayo alikuimirira pamodzi nao, analibe kanthu kakunena kotsutsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma popeza iwo amamuona munthu amene anachiritsidwa atayima pamodzi ndi iwo, palibe chimene akananena.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipotu pakuona munthu wociritsidwayoalikuimirira pamodzi nao, analibe kanthu kakunena kotsutsa.