Acts 4:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho adaŵalamula kuti atuluke m'bwalo la milandu lija, kenaka abwalowo adayamba kukambirana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma pamene anawalamulira iwo achoke m'bwalo la akulu, ananena wina ndi mnzake,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa chake anawalamula kuti atuluke mʼbwalo la milandu ndipo akulu abwalowo anayamba kukambirana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma pamene anawalamulira iwo acoke m'bwalo la akulu, ananena wina ndi mnzace,