Acts 4:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo ndalamazo ankagaŵira munthu aliyense malinga ndi kusoŵa kwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nawaika pa mapazi a atumwi; ndipo anagawira yense monga kusowa kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndi kuzipereka kwa atumwi, ndipo zimagawidwa kwa aliyense amene anali ndi chosowa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
2 nawaika pa mapazi a atumwi; ndipo anagawira yense monga kusowakwace.