Acts 4:36 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Panali munthu wina dzina lake Yosefe, wa fuko la Levi, mbadwa ya ku Kipro, amene atumwi adaamutcha Barnabasi, ndiye kuti Wolimbitsa mtima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yosefe, wotchedwa ndi atumwi Barnabasi (ndilo losandulika mwana wa chisangalalo), Mlevi, fuko lake la ku Kipro,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yosefe, wa fuko la Levi, wochokera ku Kupro amene atumwi anamutcha Barnaba, kutanthauza kuti mwana wachilimbikitso,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yosefe, wochedwa ndi atumwi Bamaba (ndilo losandulika mwana wa cisangalalo), Mlevi, pfuko lace la ku Kupro,