Acts 4:37 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nayenso adagulitsa munda wake, nabwera ndi ndalama zake kudzazipereka kwa atumwi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pokhala nao munda, anaugulitsa, nabwera nazo ndalama zake, naziika pa mapazi a atumwi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
anagulitsa munda wake ndipo anadzapereka ndalamazo kwa atumwi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pokhala nao munda, anaugulitsa, nabwera nazo ndalama zace, 3 naziika pa mapazi a atumwi.