Acts 5:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu winanso, dzina lake Ananiya, pamodzi ndi mkazi wake Safira, adagulitsa munda wao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma munthu wina dzina lake Ananiya pamodzi ndi Safira mkazi wake,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma munthu wina dzina lake Hananiya, pamodzi ndi mkazi wake Safira, anagulitsanso munda wawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma munthu wina dzina lace Hananiya pamodzi ndi Safira mkazi wace,