Acts 5:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma usiku mngelo wa Ambuye adatsekula zitseko za ndendeyo naŵatulutsa. Adaŵauza kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mngelo wa Ambuye anatsegula pakhomo pa ndende usiku, nawatulutsa, nati,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma usiku mngelo wa Ambuye anatsekula zitseko za ndende ndi kuwatulutsa
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mngelo wa Ambuye anatsegula pakhomo pa ndende usiku, nawaturutsa, nati,