Acts 5:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atafika nawo, adaŵakhazika pamaso pa Bungwe Lalikulu lija, ndipo mkulu wa ansembe onse adayamba kuŵafunsa mafunso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo m'mene adadza nao, anawaika pa bwalo la akulu. Ndipo anawafunsa mkulu wa ansembe,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atafika nawo atumwi aja, anawayimika pamaso pa Bwalo Lalikulu kuti afunsidwe mafunso ndi mkulu wa ansembe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo m'mene adadza nao, anawaika pa bwalo la akuru. Ndipo anawafunsa mkuru wa ansembe,