Acts 5:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Patapita ngati maora atatu, mkazi wake adaloŵa, osadziŵa zimene zachitika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma atapita monga maora atatu, ndipo mkazi wake, wosadziwa chidachitikacho, analowa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Patapita maora atatu mkazi wake analowa, wosadziwa zimene zinachitika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma atapita monga maora atatu, ndipo mkazi wace, wosadziwa cidacitikaco, analowa.