Acts 7:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Yakobe adamva kuti ku Ejipito kuli tirigu, adatumako makolo athu aja. Uwu unali ulendo wao woyamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma pakumva Yakobo kuti muli tirigu m'Ejipito, anatuma makolo athu ulendo woyamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Yakobo anamva kuti ku Igupto kunali tirigu, iye anatuma makolo athu ulendo woyamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma pakumva Yakobo kuti muli tirigu m'Aigupto, anatuma makolo athu ulendo woyamba,