Acts 7:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mfumuyo idachenjerera mtundu wathu, nkuyamba kuzunza makolo athu, pakuŵatayitsa ana ao akhanda kuti asakhale ndi moyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Imeneyo inachenjerera fuko lathu, niwachitira choipa makolo athu, niwatayitsa tiana tao, kuti tingakhale ndi moyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumuyo inachita mwachinyengo ndi mtundu wathu ndi kuwazunza kuti ataye ana awo akhanda kuti afe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Imeneyo inacenjerera pfuko lathu, niwacitira coipa makolo athu, niwatayitsa tiana tao, kuti tingakhale ndi moyo.