Acts 7:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iye adayankha kuti, “Abale anga ndi atate anga, mverani! Mulungu waulemerero adaonekera kholo lathu Abrahamu pamene ankakhala ku Mesopotamiya, asanakakhale ku Harani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Stefano anati, Amuna inu, abale, ndi atate, tamverani. Mulungu wa ulemerero anaonekera kwa kholo lathu Abrahamu, pokhala iye m'Mesopotamiya, asanayambe kukhala m'Harani;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Stefano anayankha kuti, “Abale ndi makolo, tamverani! Mulungu waulemerero anaoneka kwa kholo lathu Abrahamu pamene ankakhala ku Mesopotamiya, asanakakhale ku Harani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Stefano anati, Amuna inu, abale, ndi atate, tamverani. Mulungu wa ulemerero anaonekera kwa kholo lathu Abrahamu, pokhala iye m'Mesopotamiya, asanayambe kukhala m'Harana;