Acts 7:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
koma atamsiya pamtsinje paja, mwana wamkazi wa Farao adamtola, namlera ngati mwana wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo pakutayika iye, anamtola mwana wamkazi wa Farao, namlera akhale mwana wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atakamutaya, mwana wamkazi wa Farao anamutola nakamulera ngati mwana wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo pakutayika iye, anamtola mwana wamkazi wa Farao, namlera akhale mwana wace.