Acts 7:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Mose adaphunzira nzeru zonse za anthu a ku Ejipito, ndipo mau ake ndi ntchito zake zinali zamphamvu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mose anaphunzira nzeru zonse za Aejipito; nali wamphamvu m'mau ake ndi m'ntchito zake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mose anaphunzira nzeru zonse za Aigupto, ndipo anali wamphamvu mʼmawu ndi ntchito zake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Moseanaphunzira nzeru zonse za Aaigupto; nali wamphamvu m'mau ace ndi m'nchito zace.