Acts 7:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Pamene zaka zake zidafikira makumi anai, adaganiza zokayendera abale ake, Aisraele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma pamene zaka zake zinafikira ngati makumi anai, kunalowa mumtima mwake kuzonda abale ake ana a Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mose ali ndi zaka makumi anayi, anaganizira zokayendera abale ake Aisraeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma pamene zaka zace zinafikira ngati makumi anai, kunalowa mumtima mwace kuzonda abale ace ana a Israyeli,