Acts 7:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma amene adaaputa mnzakeyo adakankhira Mose kumbali nati, ‘Adakuika ndani kuti ukhale mkulu wathu ndi muweruzi wathu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma iye wakumchitira mnzake choipa anamkankha, nati, Wakuika iwe ndani mkulu ndi wotiweruzira?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma munthu amene amavutitsa mnzakeyo anakankha Mose ndipo anati, ‘Ndani anakuyika kuti ukhale wotilamulira ndi wotiweruza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma iye wakumcitira mnzace coipa anamkankha, nati, Wakuika iwe ndani mkulu ndi wotiweruzira?