Acts 7:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamuuza kuti, ‘Tuluka m'dziko lako, uŵasiye abale ako, ubwere ku dziko limene ndidzakusonyeza.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nati kwa iye, Tuluka kudziko lako ndi kwa abale ako, ndipo tiye kudziko limene ndidzakusonyeza iwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu anati, ‘Tuluka mʼdziko lako, siya abale ako, ndipo pita ku dziko limene ndidzakusonyeza.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nati kwa iye, Turuka ku dziko lako ndi kwa abale ako, ndipo tiye ku dziko limene ndidzakusonyeza iwe.