Acts 7:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mose ataona zimenezi adazizwa, ndipo adasendera pafupi kuti aonetsetse. Pamenepo adamva mau a Chauta akuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Mose pakuona, anazizwa pa choonekacho; ndipo pakuyandikira iye kukaona, kunadza mau a Ambuye,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye ataona zimenezi, anadabwa. Akupita kuti akaonetsetse pafupi, Mose anamva mawu a Ambuye:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
4 Koma Mose pakuona, anazizwa pa coonekaco; ndipo pakuyandikira iye kukaona, kunadza mau a Ambuye,