Acts 7:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
‘Ine ndine Mulungu wa makolo ako, Mulungu wa Abrahamu, Isaki, ndi Yakobe.’ Mose adayamba kunjenjemera mwakuti sadalimbenso mtima kuti nkupenyako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
akuti, Ine ndine Mulungu wa makolo anu, Mulungu wa Abrahamu, ndi wa Isaki, ndi wa Yakobo. Ndipo Mose ananthunthumira, osalimbika mtima kupenyetsako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
‘Ine ndine Mulungu wa makolo ako, Mulungu wa Abrahamu, Isake ndi Yakobo.’ Mose ananjenjemera chifukwa cha mantha ndipo sanalimbe mtima kuyangʼananso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
5 akuti, Ine ndine Mulungu wa makolo anu, Mulungu wa Abrahamu, ndi wa Isake, ndi wa Yakobo. Ndipo Mose ananthunthumira, osalimbika mtima kupenyetsako.