Acts 7:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Chauta adamuuza kuti, ‘Vula nsapato zakozo, chifukwa malo ukupondawo ngopatulika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Ambuye anati kwa iye, Masula nsapato kumapazi ako; pakuti pa malo amene upondapo mpopatulika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ndipo Ambuye anati kwa Mose, ‘Vula nsapato zako, pakuti malo amene wayimapo ndi opatulika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
6 Ndipo Ambuye anati kwa iye, Masula nsapato ku mapazi ako; pakuti pa malo amene upondapo mpopatulika.