Acts 7:39 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Koma makolo athu aja adakana kumumvera, m'malo mwake adamkankhira kumbali. Mitima yao idatembenukira za ku Ejipito.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
amene makolo athu sanafuna kumvera iye, koma anamkankha achoke, nabwerera m'mbuyo mumtima mwao ku Ejipito,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma makolo athu anakana kumumvera iye. Iwo anamukana iye ndipo mʼmitima mwawo anatembenukira ku Igupto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
amene makolo athu sanafuna kumvera iye, koma anamkankha acoke, nabwerera m'mbuyo mumtima mwao ku Aigupto,