Acts 7:45 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chihemacho chimene makolo athu adachilandira kwa makolo ao aja, adabwera nacho kuno Yoswa akuŵatsogolera pamene adalanda dziko kwa mitundu ya anthu imene Mulungu adaipitikitsa iwo akufika. Chidakhala pakati pao mpaka nthaŵi ya Davide.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chimenenso makolo athu akudza m'mbuyo, analowa nacho ndi Yoswa polandira iwo zao za amitundu, amene Mulungu anawaingitsa pamaso pa makolo athu, kufikira masiku a Davide;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Makolo athu, atayilandira Tentiyo, anabwera nayo motsogozedwa ndi Yoswa pamene analanda dziko la mitundu imene Mulungu anayipirikitsa pamaso pawo. Tentiyo inakhala mʼdzikomo mpaka nthawi ya Davide,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
17 Cimenenso makolo athu akudza m'mbuyo, analowa naco ndi Y oswa polandira iwo zao za amitundu, 18 amene Mulungu anawaingitsa pamaso pa makolo athu, kufikira masiku a Davine;