Acts 7:52 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi alipo mneneri ndi mmodzi yemwe amene makolo anu aja sadamzunze? Iyai, iwo adapha anthu amene ankaneneratu za kudza kwake kwa Wolungama uja. Tsopano inuyo mudampereka kwa adani ake ndi kumupha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiye yani wa aneneri makolo anu sanamzunza? Ndipo anawapha iwo amene anaonetseratu za kudza kwake kwa Wolungamayo; wa Iye amene mwakhala tsopano akumpereka ndi akumupha;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi analipo mneneri amene makolo anu sanamuzunze? Iwo anapha ngakhale amene ananeneratu za kubwera kwa Wolungamayo. Ndipo tsopano inu munamupereka ndi kumupha Iye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
23 ndiye yani wa aneneri makolo anu sanamzunza? ndipo anawapha iwo amene anaonetseratu za kudzakwace kwa Wolungamayo; wa iye amene mwakhala tsopano akumpereka ndi akumupha;